Standard Bank yatha Bullets osawinako Bank ya Standard yalengeza kuti yasiya kupanga sponsor Standard Bank Knockout Cup
By Unknown - February 08, 2016
Standard Bank yatha Bullets osawinako
Bank ya Standard yalengeza kuti yasiya kupanga sponsor Standard Bank Knockout Cup kuyambira lero kamba ka mavuto a za chuma omwe akula kwambiri m'dziko muno.
Iwo ati momwe chiliri chuma cha dziko lino, bank imeneyi ikuvutika kuti idziyenda bwino ndipo yaganiza zongosiya.
Zateremu, team ya Big Bullets yomwe sinatengepo chikho chimenechi chiyambileni pomwe chinayamba mu 2007 sidzachionanso.
Ma team omwe amwemwetera ndi Mighty Wanderers, Silver Strikers, Azam Tigers, Civo, Blue Eagles ndi Moyale Barracks omwe atengapo chikhochi....
0 comments