Super League Association of Malawi (Sulom) .
By Unknown - April 19, 2016
Super League Association of Malawi (Sulom) .
Yati Mateam aWizard Fc komaso Karonga united ndiwo ma team amwe akhale akusewela nawo masewelo amu 2016 TNM Premier League .
Karonga United yapatsidwa mpata umenewu kamba kakulephela kwa team ija ya Chilumba Barrack izi ndimalingana ndi bungwe la Sulom.
Pomwe team ya Wizard Fc yapatsidwa mpatawu maka kamba kopambana pamasewelo omwe anagonjetsa Airborn fc pama play off izi zatengelaso kusatenga nawo mbali kwa team ija ya Dedza Young Soccer.
Zatelemu ndiye kuti zatsimikiza tsopano kuti league ya TNM mchaka chino ikhala ndi ma team Khumi Asanu ndi imodzi (16)
0 comments