Dear atsikana ndi azimayi tivelaneko ndipo ndi nkhani yofunikila osanyozelayi.
By Unknown - February 16, 2018
Nd
Mulungu kunkhani yosunga Moyo imeneyo ndi khani zina zazikulu chifukwa tonsefe amatisungila moyo
ndi mulungu ndi kunena kumbali zina tsopano.akazi tiyenela kukhala athu achikondi ndi azimuna athu kuwamvetsetsa kuwamvela kukhala odekha awulemu ngakhale palikusagwiri zana panthawi yoti tamupeza mamunawathu ndivuto kuti watilakwila choyamba amai ngati mwamva nkhani kapena mwapeza zolakwika za mamunanu kuti sizinakusangala
zakukhumudwitsa
0 comments