Abale ndi alongo tonse kumene tiriko, ine ndikufuna ndikutsekuleniko mutu pang'ono ena ndikudziwa simgwirizana nane koma muona paumuthu kut ndikukamba zoona, siine wandale kapena kusapota wina wake ayi !!
Koma ndati ndikufunseni inuyo pamene mulipo pazimene mwamva zoti Bushiri wagwirizana ndi apolice kapena boma la south Africa kut agwire aliyese mmalawi apite kukamvotera kumalawi,
Amalawi tatiyeni tione kaye kut, andale pokopa anthu kut awavotere amapanga bwanji? Amawakakamiza or kuwanyengerera????
Or kupanda kuganizako zoona muthu kuvotera muthu chifukwa cha matha? ????
Dziwani ichi Amalawi, iyi ndi propaganda imene I kuchokera kuzipani zomwe zikuopa kut Bushiri akaimira upresident inuyo kapena abale anu asakamvotere,
Chilungamo ndichoti, apolice akugwiradi maforeigner ku South Africa osati Amalawi okha! !!! Koma msanamizidwe kut achita kutumidwa ndi Bushiri kugwira Amalawi okha ayi,zikanakhala zomveka akananena kut kuli mabus otenga athu kupita nao ku Malawi ndikubwera nao ku south Africa! !! Osati akugwireni apolice akudzudzeni kukupatsani kumalawi mkamvotere iyeyu ayi ndithu!
Monga ndanena kale ine ndiribe chipani koma kumene muliko amene mwamva ma audios ndi mamessages osokonedzawa kut mufune msafune apolice akugwirani kukutumizani kumalawi kuli mabus ow atenga athu, Boza lenileni lochokera mkamwa mwa satana ndipo inuyo ngat mukupitiriza ndizimenezi ziwani kut mkulakwa chifukwa sizoona
Uthengau pangan forward kwa anzanu ndi magulu osiyana siyana muwatsegule maso, chifukwa mau a Mulungu akuti, Anthu anga akuonongeka chifukwa cha kusadziwa
God bless you as you share today! !!!!🙏🏻🙏🏻
0 comments