Ukakumana ndi Yesu Sukhara cimozmozi
Moses anagawa nyanja Ana Israel naoloka powuma,pomwe panari chotchinga Mulungu anapeleka kuthekera.
Yesu sanagawe nyanja koma kuyenda pa mwamba pa Mazi.
Nyanja yanu ndimavuto omwe mukuwaona kukhara akulu ,omwe ayamba kukumizan mwina ndinthenda ,kusowa tchito,mpamba,banja,Ana vuto lililotse mukumana nalo ndiye nyanja Yanu .
Tsono Yese Anamulandira Yesu anapatsa mphamvu yakukhara Ana Amulungu.
Muli mphamvu ngati Yesu yakuyenda pa mwamba pa vuto lililotse,muli mphamvu yolamulira Vuto lililotse chifukwa muli mphamvu ndi ulamuliro
Chachikulu kukumana nae Yesu .
ndikumulora kukhara moyo wanu ,ndikulamulira chilichotse cha Moyo wanu.
Chilichotse chotheka vuto limakura ngati .
Lili ndimphamvu kupotsa Iwe.
Ngati layamba kukumizani,koma wa Yesu samizidwa popeza iye Ali mphamvu yakumiza kuyenda pa mwamba pa vuto lililotse.
Muziwen Yesu,ziwani udindo ndi ulamuliro mwanyamura otsalora vuto kuliona kukula kupotsa Yesu wanu ,muloleni Yesu akumenyeleni nkhondo yotse ,zosatheka ndinu zimatheka ndi Iye
0 comments