Dear atsikana ndi azimayi tivelaneko ndipo ndi nkhani yofunikila osanyozelayi.

By Unknown - February 16, 2018




Dear atsikana ndi azimayi tivelaneko ndipo ndi nkhani yofunikila osanyozelayi.

Nd
i manena nthawi zonse kumakhalidwe anyumba mwanumo kapena kumbali yamakhalidwe ngati ulindi chibwezi chomwe chikufuna kudzakukwatila. Ife akazi ndi osunga moyo wa azimuna athu chifukwa timawasamalila tsiku ndi tsiku. Mundi vetsetsetu apa posunga moyopa paja enanu kuvetsetsa kumakuvutani mumayamba kutembenuza nkhani sindi kunenatu kuti tingamupose Mulungu kunkhani yosunga Moyo imeneyo ndi khani zina zazikulu chifukwa tonsefe amatisungila moyo ndi mulungu ndi kunena kumbali zina tsopano.akazi tiyenela kukhala athu achikondi ndi azimuna athu kuwamvetsetsa kuwamvela kukhala odekha awulemu ngakhale palikusagwiri zana panthawi yoti tamupeza mamunawathu ndivuto kuti watilakwila 


choyamba amai ngati mwamva nkhani kapena mwapeza zolakwika za mamunanu kuti sizinakusangalatseni chonde musafuse mwaphuma ai ngati alikuntchito musamuyimbire fone kapena kutuma mesege ai mudikilileni abwela kuntchitoko olo kulikonse komwe wapitako akabwela osawonetsa nkhope yokwiya ai musiyeni alowe nyumba ndipo akhalepansi apume mupatseni madzi osamba akamabwela apeze chakudya akamaliza nde mumuyitane kuchipinda mwaulemu ndi chikondi mumupatse moni kuti mwaswela bwanji nanga 

mwayenda bwanji ndemutha kuyamba kufusako ndi zomwe zakukhumudwitsani mosakweza mau kapena kumutosa chala ndipo musadzayelekeze kumufusa mwamwano amuna amadana nazo zimenezo muyesetse kuti mwakambirana mwa bata ndi mtendele.china mukakangana pakhomo ndi amuna anu musakwiyile aliyense obwela pakhomopo chifukwa zanuzo sizikuwakhudza musadzayelekeze kuyang'ana mufoni ya amuna anu kapena chibwezi chanu atachoka kukasamba opanda ulamulilo wake mudzidza ngokhalila kuyambana osamumana chakudya mamuna chifukwa mwayambana mukuti kufuna kumuwonetsa kuti mwakwiya ai osamukaniza mamuna kukugwilani kubediko chifukwa mwakwiya mamuna olo mutalakwa muli inuyo kumutha kwake ndi kugona opanda kanthu sangakusiye chifukwa nde kudya kwake osamulondola kumowa tavana

  • Share:

You Might Also Like

0 comments