Mdzina la Yesu, Yehova tikuyamikani chifukwa cha zifundo ndi zisomo zanu paife, komaso chifukwa cha kutikondela kwapaderadera, mulemekezeke Ambuye.
...
Tikupemphani kuti mutsogolele zinthu zathu zonse pamoyo wapansi pano, kuti tiziyenda mzisomo zanu ndikupindulitsa ena komanso ntchito zamanja athu, tithangatileni kusunga chiyelo mmaendedwe athu onse kuti tidzaone nkhope yanu, popeza ndiokhaowo oyera mtima omwe adzaona inu Yehova.
...
Limbanani ndi zolimbana nafe, menyanani ndi zomenyana nafe monga mwa mau anu pa MASALMO 35:1,8. Mu mdzina la Yesu
Tapemphera #AMEEEN
0 comments