NDIULULE PANG'ONO POKHA

By Unknown - February 21, 2018




NDIULULE PANG'ONO POKHA
Umu ndmene DPP inasithira nzin2 M'malawi muno
1. Zipatala monga Mzuzu Central, Kamuzu Central ndi queens zinali za ulele koma pano kungolembetsa mankhwala ndi K1,500.
2. Fertilizer wa macupon timagula K500, per bag pano tikugula K16,000 per bag.
3. Passport timapangitsa K15,000 pano K60,000.
4. Timakhomera driving license pa K5,000, pano ndi K60,000.
5, Kunalibe ma strikes pano akumamangidwa now and then
6. Timakhala ndi magetsi 24hours pano tikukhala ndi mdima 24hours.
7.Nthito sizinkavuta, pano ma graduates ambiri ndi migwanya.
8. After graduated to university unkapita direct kukalembedwa ntchito pano zikumafunika kupanga Kaye apply, kusakasaka Kaye nthito
9.Ma TTC onse aboma anali aulele, kubwera kwa inu tayamba kulipira fees K30,000.
10.Ma business ankayenda bwino, pano sakuyenda because of magetsi komanso a city akumathamangitsa.
11. Amuluzi anabweretsa free primary education, nanga Zoti mwana wa primary azilipira K1,700 ya school fund zabwera bwanji?
12. Kodi polamula kuti ofuna kubwereza form 4 azikayambiranso form 1, mukufuna osaukafe tiphunzire kapena tizafe ndi umbuli wathu?
Zositha ndi zambiri zatchulidwaz ndi 12% chabe

  • Share:

You Might Also Like

0 comments