GENESIS 41:37-57. ...

By Unknown - March 03, 2018







GENESIS 41:37-57.
...
Nkhan yake ndiya Ulamuliro Wa Yosefe Mudziko La Aigupto.
Yosefe ndi Nyamata Amene Anasalidwa kwambiri ndi abale ake Kamba Ka # MALOTO , Mpaka anaganiza zomupha komwa mwa mwai anaona kagulu kena komwe kamanka nagula akapolo ndipo anamugulisa Kukhala Kapolo Kudziko Lakutal.
...
Momwe Yosefe Ankagulitsdwa nkutu ali ndizaka 17 ndipo anaki kudusa munyengo zovuta, Mpaka Kuponyedwa Ndende Pazinthu Zoti Sanapange koma Kaamba Kacilungamo, ankachita chifuniro cha Mulungu, Angakhale zinali chomwechi iye Sananyonze Mulungu, Kufikira anamasulira Maloto anyamata awiri Mundende.
...
Ndpo Znacitikadi Mwakumasulira Kwake Koma Satana Anamukhomererabe, Izi Sizinasunthe Cikhulupiriro Chake Kufkira Mulungu Anapereka Ulemerero Wake Umene Unayamba M'maloto Mkumaliziranso M'maloto,pomasu
lira Maloto A Farao Nthawi Iyi Ali Ndi Zaka 30.
...
M'bale Mulungu sanyozeka, angakhale zitavuta maka koma dzina ili lokha usanyoze kaamba koti ukudutsa munyengo zovuta, Mkutheka Inunso Ntchito/Banja Lanu Linatha, Abale,anzanu, Anasiya Kukuyankhulan Kaamba koti ndinu osapata, ndiinu otsauka kiphatizikiza apo mumanenanso chilungamo mumakhazikika pachoonadi, Musade nkhawa Mulungu sanakuiwaleni, limbikanibe mpaka ukulu wake uonekere pa inu. Zilibe kanthu kuti mabvuto sakukuchokan, Mot Mumafika Kuziyankhulira Nokha Kut Munabadwiranji,lero Mau Akut Limbikanbe Kukhulupirira YEHOVA Ndkudalira Paiye Nyengo Zonse Ndpo Abwenz Anakuthawanio Azakugwadiran, YOBU 19 VS 19 AKUTI ABWENZI ANGA ENI ENI ONSE ANYATSIDWA NANE NDI ONSE NDAKONDANA NAO ASANDULIKA ADANI ANGA" dziko lapansi limatero abwenz amachukuka ukakhala pa ntendere koma ukakhala muzovuta amabalalika, amakhala abusy phone yako samaiyankha, chomwe amadikira nchoti amve kuti wamwalira nao umphawiwo, iwo azagule bokosi, azatamike pakupeleka chipepetso, koma ndithandizo lakumwamba sizitheka mudzina la Yesu mpaka atazaona ulemekero wako.

  • Share:

You Might Also Like

0 comments