­
­

Dzulo Ndinali Ku Ukwati Wa Ex Girlfriend Wanga.

By Unknown - February 23, 2018



Dzulo Ndinali Ku Ukwati Wa Ex Girlfriend Wanga. Then Pa Nthawi Yoti Alumbile Samadziwa Kuti Ndinali Ku Church Konko, Atamufusa Abusa Kuti Ukulumbila Zoti Udzakhala Mkazi Wa..........Mpaka Kufikila Imfa Yako??? Kenaka Anatembenuka Ndikundiona Posakhalitsa Anapukusa Mutu Kwinaku Akulututsa Misonzi, Koma Maso Ake Ali Kwa Ine Kufikila Abusa Kudabwa Komanso Mamuna Wake Ndi Makolo ake. "Ndi....Ndi....Ndi...... Kenaka Anagwa Pansi Mkukomoka Nthawi Yomweyo. Ineso Nditaona Kuti Ex Wanga Wakomoka, Naneso Ndinangogwa PODZUKA NDANGOZINDIKILA KUTI NDAGWA PA BED ANALI MALOTO..

  • Share:

You Might Also Like

0 comments